Yoswa 22:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Wansembe Pinihasi, atsogoleri a gulu la Aisiraeli ndiponso atsogoleri a masauzande a Aisiraeli amene anali naye, atamva mawu amene ana a Rubeni, a Gadi ndi a Manase ananena, anakhutira.+
30 Wansembe Pinihasi, atsogoleri a gulu la Aisiraeli ndiponso atsogoleri a masauzande a Aisiraeli amene anali naye, atamva mawu amene ana a Rubeni, a Gadi ndi a Manase ananena, anakhutira.+