-
Yoswa 22:31Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
31 Ndiyeno Pinihasi mwana wa wansembe Eliezara, anauza ana a Rubeni, a Gadi ndi a Manase, kuti: “Lero tadziwa kuti Yehova ali pakati pathu chifukwa simunachite zosakhulupirika kwa Yehova. Apatu mwapulumutsa Aisiraeli mʼdzanja la Yehova.”
-