Yoswa 23:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Yoswa anaitana Aisiraeli onse,+ akulu awo, atsogoleri, oweruza ndi akapitawo+ nʼkuwauza kuti: “Ine ndakalamba ndipo ndili ndi zaka zambiri. Yoswa Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 23:2 Nsanja ya Olonda,7/1/1992, tsa. 12
2 Yoswa anaitana Aisiraeli onse,+ akulu awo, atsogoleri, oweruza ndi akapitawo+ nʼkuwauza kuti: “Ine ndakalamba ndipo ndili ndi zaka zambiri.