Yoswa 23:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndinakupatsani malo a mitundu yonse imene yatsalayi pochita maere.+ Ndinakupatsaninso malo a mitundu imene ndinaiwononga+ kuchokera kumtsinje wa Yorodano mpaka ku Nyanja Yaikulu* chakumadzulo,* kuti akhale cholowa cha mafuko anu.+
4 Ndinakupatsani malo a mitundu yonse imene yatsalayi pochita maere.+ Ndinakupatsaninso malo a mitundu imene ndinaiwononga+ kuchokera kumtsinje wa Yorodano mpaka ku Nyanja Yaikulu* chakumadzulo,* kuti akhale cholowa cha mafuko anu.+