Yoswa 23:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Yehova Mulungu wanu ndi amene ankawachotsa pamaso panu,+ ndipo anawathamangitsa chifukwa cha inu. Inu munatenga malo awo mogwirizana ndi zimene Yehova Mulungu wanu anakulonjezani.+
5 Yehova Mulungu wanu ndi amene ankawachotsa pamaso panu,+ ndipo anawathamangitsa chifukwa cha inu. Inu munatenga malo awo mogwirizana ndi zimene Yehova Mulungu wanu anakulonjezani.+