Yoswa 23:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Tsopano limbani mtima kwambiri kuti muzitsatira zonse zimene zinalembedwa mʼbuku la Chilamulo+ cha Mose, ndipo musapite kudzanja lamanja kapena lamanzere.+
6 Tsopano limbani mtima kwambiri kuti muzitsatira zonse zimene zinalembedwa mʼbuku la Chilamulo+ cha Mose, ndipo musapite kudzanja lamanja kapena lamanzere.+