Yoswa 23:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndiponso muzipewa kugwirizana* ndi mitundu+ imene yatsala pakati panu. Musamatchule nʼkomwe mayina a milungu yawo+ kapena kulumbira pa milunguyo, ndipo musamaitumikire kapena kuigwadira.+
7 Ndiponso muzipewa kugwirizana* ndi mitundu+ imene yatsala pakati panu. Musamatchule nʼkomwe mayina a milungu yawo+ kapena kulumbira pa milunguyo, ndipo musamaitumikire kapena kuigwadira.+