Yoswa 23:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Koma muyenera kumamatira Yehova Mulungu wanu+ ngati mmene mwakhala mukuchitira mpaka lero.