Yoswa 23:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Munthu mmodzi yekha wa inu adzathamangitsa anthu 1,000,+ chifukwa Yehova Mulungu wanu akukumenyerani nkhondo+ mogwirizana ndi zimene anakulonjezani.+
10 Munthu mmodzi yekha wa inu adzathamangitsa anthu 1,000,+ chifukwa Yehova Mulungu wanu akukumenyerani nkhondo+ mogwirizana ndi zimene anakulonjezani.+