Yoswa 24:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Kenako Yoswa anasonkhanitsa mafuko onse a Isiraeli ku Sekemu. Iye anaitanitsa akulu a Isiraeli, atsogoleri, oweruza ndi akapitawo+ ndipo onse anaima pamaso pa Mulungu woona. Yoswa Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 24:1 Nsanja ya Olonda,7/1/1992, tsa. 12
24 Kenako Yoswa anasonkhanitsa mafuko onse a Isiraeli ku Sekemu. Iye anaitanitsa akulu a Isiraeli, atsogoleri, oweruza ndi akapitawo+ ndipo onse anaima pamaso pa Mulungu woona.