Yoswa 24:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Yoswa anauza anthuwo kuti: “Yehova Mulungu wa Isiraeli wanena kuti, ‘Kale makolo anu,+ kuphatikizapo Tera, bambo ake a Abulahamu ndi Nahori, ankakhala kutsidya lina la Mtsinje,*+ ndipo ankatumikira milungu ina.+ Yoswa Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 24:2 Tsanzirani, tsa. 25 Nsanja ya Olonda,12/1/2004, tsa. 118/15/2001, ptsa. 14-15
2 Yoswa anauza anthuwo kuti: “Yehova Mulungu wa Isiraeli wanena kuti, ‘Kale makolo anu,+ kuphatikizapo Tera, bambo ake a Abulahamu ndi Nahori, ankakhala kutsidya lina la Mtsinje,*+ ndipo ankatumikira milungu ina.+