Yoswa 24:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Patapita nthawi ndinatumiza Mose ndi Aroni+ ndipo ndinachititsa kuti ku Iguputo kugwe miliri.+ Kenako ndinakutulutsani ku Iguputoko.
5 Patapita nthawi ndinatumiza Mose ndi Aroni+ ndipo ndinachititsa kuti ku Iguputo kugwe miliri.+ Kenako ndinakutulutsani ku Iguputoko.