Yoswa 24:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pamene ndinkatulutsa makolo anu ku Iguputo,+ atatsala pangʼono kufika kunyanja, Aiguputo anawathamangira ndi magaleta ankhondo ndiponso amuna okwera pamahatchi, mpaka ku Nyanja Yofiira.+
6 Pamene ndinkatulutsa makolo anu ku Iguputo,+ atatsala pangʼono kufika kunyanja, Aiguputo anawathamangira ndi magaleta ankhondo ndiponso amuna okwera pamahatchi, mpaka ku Nyanja Yofiira.+