Yoswa 24:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Iwo anayamba kufuulira Yehova.+ Choncho ndinaika mdima pakati pa iwo ndi Aiguputuwo, ndipo ndinawamiza ndi madzi amʼnyanja.+ Munaona ndi maso anu zimene ndinachita ku Iguputo.+ Kenako inu munakhala mʼchipululu zaka zambiri.*+
7 Iwo anayamba kufuulira Yehova.+ Choncho ndinaika mdima pakati pa iwo ndi Aiguputuwo, ndipo ndinawamiza ndi madzi amʼnyanja.+ Munaona ndi maso anu zimene ndinachita ku Iguputo.+ Kenako inu munakhala mʼchipululu zaka zambiri.*+