Yoswa 24:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kenako Balaki mwana wa Zipori, mfumu ya Mowabu, ananyamuka kukamenyana ndi Aisiraeli. Iye anaitanitsa Balamu, mwana wa Beori kuti akutemberereni.+
9 Kenako Balaki mwana wa Zipori, mfumu ya Mowabu, ananyamuka kukamenyana ndi Aisiraeli. Iye anaitanitsa Balamu, mwana wa Beori kuti akutemberereni.+