Yoswa 24:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Koma ine sindinafune kumvera Balamu.+ Choncho iye anakudalitsani mobwerezabwereza+ ndipo ndinakulanditsani mʼmanja mwake.+
10 Koma ine sindinafune kumvera Balamu.+ Choncho iye anakudalitsani mobwerezabwereza+ ndipo ndinakulanditsani mʼmanja mwake.+