Yoswa 24:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ndinakupatsani dziko limene simunalikhetsere thukuta komanso mizinda imene simunaimange,+ ndipo munayamba kukhalamo. Mukudyanso zipatso za mitengo ya mpesa ndi mitengo ya maolivi imene simunadzale.’+
13 Ndinakupatsani dziko limene simunalikhetsere thukuta komanso mizinda imene simunaimange,+ ndipo munayamba kukhalamo. Mukudyanso zipatso za mitengo ya mpesa ndi mitengo ya maolivi imene simunadzale.’+