Yoswa 24:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Choncho muziopa Yehova ndi kumʼtumikira ndi mtima wathunthu* komanso mokhulupirika.*+ Chotsani milungu imene makolo anu ankatumikira kutsidya lina la Mtsinje* ndi ku Iguputo,+ ndipo muzitumikira Yehova.
14 Choncho muziopa Yehova ndi kumʼtumikira ndi mtima wathunthu* komanso mokhulupirika.*+ Chotsani milungu imene makolo anu ankatumikira kutsidya lina la Mtsinje* ndi ku Iguputo,+ ndipo muzitumikira Yehova.