Yoswa 24:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ndiyeno Yoswa anauza anthuwo kuti: “Simungathe kutumikira Yehova, chifukwa iye ndi Mulungu woyera.+ Iye ndi Mulungu amene amafuna kuti anthu azidzipereka kwa iye yekha.+ Sadzakhululuka zolakwa zanu* ndi machimo anu.+
19 Ndiyeno Yoswa anauza anthuwo kuti: “Simungathe kutumikira Yehova, chifukwa iye ndi Mulungu woyera.+ Iye ndi Mulungu amene amafuna kuti anthu azidzipereka kwa iye yekha.+ Sadzakhululuka zolakwa zanu* ndi machimo anu.+