Yoswa 24:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Choncho Yoswa anauza anthuwo kuti: “Mukudzichitira umboni wotsimikizira kuti mwasankha nokha kutumikira Yehova.”+ Ndiyeno anthuwo anati: “Inde! Ndife mboni.”
22 Choncho Yoswa anauza anthuwo kuti: “Mukudzichitira umboni wotsimikizira kuti mwasankha nokha kutumikira Yehova.”+ Ndiyeno anthuwo anati: “Inde! Ndife mboni.”