Yoswa 24:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Yoswa anauza anthu onsewo kuti: “Mwauona mwalawu? Mwala umenewu ukhala mboni yathu,+ chifukwa wamva mawu onse amene Yehova watiuza, ndipo ukhala mboni yanu kuti musadzakane Mulungu wanu.”
27 Yoswa anauza anthu onsewo kuti: “Mwauona mwalawu? Mwala umenewu ukhala mboni yathu,+ chifukwa wamva mawu onse amene Yehova watiuza, ndipo ukhala mboni yanu kuti musadzakane Mulungu wanu.”