Yoswa 24:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Nayenso Eleazara mwana wa Aroni anamwalira.+ Choncho anamuika mʼmanda mʼphiri la Pinihasi mwana wake,+ limene anapatsidwa mʼdera lamapiri la Efuraimu.
33 Nayenso Eleazara mwana wa Aroni anamwalira.+ Choncho anamuika mʼmanda mʼphiri la Pinihasi mwana wake,+ limene anapatsidwa mʼdera lamapiri la Efuraimu.