Oweruza 1:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Yehova anayankha kuti: “Ayambe Yuda,+ ndipo ndapereka* dzikolo mʼmanja mwake.” Oweruza Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:2 Nsanja ya Olonda,1/15/2005, tsa. 24