Oweruza 1:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Zitatero, Adoni-bezeki anati: “Pali mafumu 70 odulidwa zala zazikulu zamʼmanja ndi zakumapazi, amene ankatola chakudya pansi pa tebulo langa. Mulungu wandibwezera zimene ndinachita.” Kenako anamʼtengera ku Yerusalemu+ kumene anakafera.
7 Zitatero, Adoni-bezeki anati: “Pali mafumu 70 odulidwa zala zazikulu zamʼmanja ndi zakumapazi, amene ankatola chakudya pansi pa tebulo langa. Mulungu wandibwezera zimene ndinachita.” Kenako anamʼtengera ku Yerusalemu+ kumene anakafera.