Oweruza 1:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Amuna a fuko la Yuda anamenyananso ndi mzinda wa Yerusalemu+ nʼkuulanda. Anapha anthu okhala mmenemo ndi lupanga, ndipo mzindawo anautentha ndi moto. Oweruza Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:8 Mawu a Mulungu, ptsa. 95-96
8 Amuna a fuko la Yuda anamenyananso ndi mzinda wa Yerusalemu+ nʼkuulanda. Anapha anthu okhala mmenemo ndi lupanga, ndipo mzindawo anautentha ndi moto.