Oweruza 1:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Choncho fuko la Yuda linapita kukamenyana ndi Akanani amene ankakhala ku Heburoni, (poyamba dzina la mzinda wa Heburoni linali Kiriyati-ariba). Iwo anapha Sesai, Ahimani ndi Talimai.+
10 Choncho fuko la Yuda linapita kukamenyana ndi Akanani amene ankakhala ku Heburoni, (poyamba dzina la mzinda wa Heburoni linali Kiriyati-ariba). Iwo anapha Sesai, Ahimani ndi Talimai.+