Oweruza 1:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ndipo Otiniyeli+ mwana wa Kenazi,+ mngʼono wake wa Kalebe, analanda mzindawo. Choncho Kalebe anamʼpatsa Akisa mwana wake kuti akhale mkazi wake.
13 Ndipo Otiniyeli+ mwana wa Kenazi,+ mngʼono wake wa Kalebe, analanda mzindawo. Choncho Kalebe anamʼpatsa Akisa mwana wake kuti akhale mkazi wake.