Oweruza 1:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Iye anapempha kuti: “Ndidalitseni, poti mwandipatsa malo akumʼmwera* mundipatsenso Guloti-maimu.”* Choncho Kalebe anamʼpatsa Guloti Wakumtunda ndi Guloti Wakumunsi.
15 Iye anapempha kuti: “Ndidalitseni, poti mwandipatsa malo akumʼmwera* mundipatsenso Guloti-maimu.”* Choncho Kalebe anamʼpatsa Guloti Wakumtunda ndi Guloti Wakumunsi.