Oweruza 1:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Koma fuko la Yuda linayendabe ndi abale awo a fuko la Simiyoni, ndipo anapha Akanani okhala ku Zefati nʼkuwononga mzindawo.+ Choncho mzindawo anaupatsa dzina loti Horima.*+
17 Koma fuko la Yuda linayendabe ndi abale awo a fuko la Simiyoni, ndipo anapha Akanani okhala ku Zefati nʼkuwononga mzindawo.+ Choncho mzindawo anaupatsa dzina loti Horima.*+