Oweruza 1:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Yehova anali ndi fuko la Yuda moti linalanda dera lamapiri. Koma silinathe kuthamangitsa anthu okhala mʼchigwa chifukwa chakuti anthuwo anali ndi magaleta ankhondo okhala ndi zitsulo zazitali komanso zakuthwa.+
19 Yehova anali ndi fuko la Yuda moti linalanda dera lamapiri. Koma silinathe kuthamangitsa anthu okhala mʼchigwa chifukwa chakuti anthuwo anali ndi magaleta ankhondo okhala ndi zitsulo zazitali komanso zakuthwa.+