Oweruza 1:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Anapereka Heburoni kwa Kalebe ngati mmene Mose analonjezera,+ ndipo Kalebe anathamangitsa ana atatu aamuna a Anaki+ amene ankakhala kumeneko.
20 Anapereka Heburoni kwa Kalebe ngati mmene Mose analonjezera,+ ndipo Kalebe anathamangitsa ana atatu aamuna a Anaki+ amene ankakhala kumeneko.