Oweruza 1:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Anthu a fuko la Benjamini sanathamangitse Ayebusi a ku Yerusalemu, moti Ayebusiwo akukhalabe ndi anthu a fuko la Benjamini ku Yerusalemu mpaka lero.+ Oweruza Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:21 Mawu a Mulungu, ptsa. 95-96
21 Anthu a fuko la Benjamini sanathamangitse Ayebusi a ku Yerusalemu, moti Ayebusiwo akukhalabe ndi anthu a fuko la Benjamini ku Yerusalemu mpaka lero.+