Oweruza 1:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ndiyeno anthu amene ankafufuzawo anaona mwamuna wina akutuluka mumzindawo, ndipo anamuuza kuti: “Tiuze mmene tingalowere mumzinda, ndipo tikukomera mtima.”*
24 Ndiyeno anthu amene ankafufuzawo anaona mwamuna wina akutuluka mumzindawo, ndipo anamuuza kuti: “Tiuze mmene tingalowere mumzinda, ndipo tikukomera mtima.”*