Oweruza 1:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Iye anawauzadi mmene angalowere mumzindawo, ndipo iwo anapha anthu amumzindawo ndi lupanga, koma mwamunayo ndi anthu onse a mʼbanja lake sanawaphe.+
25 Iye anawauzadi mmene angalowere mumzindawo, ndipo iwo anapha anthu amumzindawo ndi lupanga, koma mwamunayo ndi anthu onse a mʼbanja lake sanawaphe.+