Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Oweruza 1:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Manase sanatenge mzinda wa Beti-seani ndi midzi yake yozungulira komanso Taanaki+ ndi midzi yake yozungulira. Sanathamangitsenso anthu okhala mumzinda wa Dori ndi midzi yake yozungulira, anthu amumzinda wa Ibuleamu ndi midzi yake yozungulira ndi anthu okhala mumzinda wa Megido ndi midzi yake yozungulira.+ Akananiwo anakakamirabe kukhala mʼdziko limeneli.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena