Oweruza 1:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Fuko la Efuraimu nalonso silinathamangitse Akanani amene ankakhala ku Gezeri, moti Akananiwo anapitiriza kukhala pakati pawo ku Gezeriko.+
29 Fuko la Efuraimu nalonso silinathamangitse Akanani amene ankakhala ku Gezeri, moti Akananiwo anapitiriza kukhala pakati pawo ku Gezeriko.+