33 Fuko la Nafitali silinathamangitse anthu okhala mʼmizinda ya Beti-semesi ndi Beti-anati,+ koma iwo anapitiriza kukhala pakati pa Akanani akumeneko.+ Ndipo fuko la Nafitali linayamba kugwiritsa ntchito yaukapolo anthu okhala mʼmizinda ya Beti-semesi ndi Beti-anati.