Oweruza 1:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Choncho Aamori anakakamira kukhala mʼphiri la Herese ndi mʼmizinda ya Aijaloni+ ndi Saalibimu.+ Koma ana a Yosefe atayamba kukula mphamvu, anayamba kugwiritsa ntchito yaukapolo Aamoriwo.
35 Choncho Aamori anakakamira kukhala mʼphiri la Herese ndi mʼmizinda ya Aijaloni+ ndi Saalibimu.+ Koma ana a Yosefe atayamba kukula mphamvu, anayamba kugwiritsa ntchito yaukapolo Aamoriwo.