Oweruza 2:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Inuyo musachite pangano ndi anthu okhala mʼdzikoli,+ ndipo mugwetse maguwa awo ansembe.’+ Koma inu simunamvere mawu anga.+ Nʼchifukwa chiyani mwachita zimenezi?
2 Inuyo musachite pangano ndi anthu okhala mʼdzikoli,+ ndipo mugwetse maguwa awo ansembe.’+ Koma inu simunamvere mawu anga.+ Nʼchifukwa chiyani mwachita zimenezi?