Oweruza 2:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Koma woweruza akamwalira, iwo ankayambiranso kuchita zoipa kuposa makolo awo. Ankatsatira milungu ina, kuitumikira ndi kuigwadira.+ Iwo sanasiye zochita zawozo ndiponso unkhutukumve wawo.
19 Koma woweruza akamwalira, iwo ankayambiranso kuchita zoipa kuposa makolo awo. Ankatsatira milungu ina, kuitumikira ndi kuigwadira.+ Iwo sanasiye zochita zawozo ndiponso unkhutukumve wawo.