-
Oweruza 2:23Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
23 Choncho, Yehova analola mitundu imeneyi kukhalabe. Sanaithamangitse mwamsanga komanso sanaipereke mʼmanja mwa Yoswa.
-