Oweruza 3:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mulungu anagwiritsa ntchito mitunduyi poyesa Aisiraeli kuti aone ngati adzamvere malamulo amene Yehova anapereka kwa makolo awo kudzera mwa Mose.+
4 Mulungu anagwiritsa ntchito mitunduyi poyesa Aisiraeli kuti aone ngati adzamvere malamulo amene Yehova anapereka kwa makolo awo kudzera mwa Mose.+