Oweruza 3:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Zitatero Yehova anakwiyira kwambiri Aisiraeli, moti anawapereka* kwa Kusani-risataimu, mfumu ya Mesopotamiya.* Aisiraeli anatumikira Kusani-risataimu zaka 8.
8 Zitatero Yehova anakwiyira kwambiri Aisiraeli, moti anawapereka* kwa Kusani-risataimu, mfumu ya Mesopotamiya.* Aisiraeli anatumikira Kusani-risataimu zaka 8.