Oweruza 3:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mzimu wa Yehova unkamuthandiza+ ndipo anakhala woweruza wa Isiraeli. Atapita kunkhondo, Yehova anapereka Kusani-risataimu mfumu ya Mesopotamiya* mʼmanja mwake, moti anamugonjetsa.
10 Mzimu wa Yehova unkamuthandiza+ ndipo anakhala woweruza wa Isiraeli. Atapita kunkhondo, Yehova anapereka Kusani-risataimu mfumu ya Mesopotamiya* mʼmanja mwake, moti anamugonjetsa.