Oweruza 3:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Aisiraeli anayambiranso kuchita zoipa pamaso pa Yehova.+ Choncho Yehova analola Egiloni mfumu ya Mowabu+ kuti azipondereza Aisiraeli, chifukwa anachita zoipa pamaso pa Yehova.
12 Aisiraeli anayambiranso kuchita zoipa pamaso pa Yehova.+ Choncho Yehova analola Egiloni mfumu ya Mowabu+ kuti azipondereza Aisiraeli, chifukwa anachita zoipa pamaso pa Yehova.