Oweruza 3:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Kuwonjezera apo, anachititsa kuti Aamoni+ ndi Aamaleki+ alimbane ndi Aisiraeli. Iwo anamenyana ndi Aisiraeliwo nʼkulanda mzinda wa mitengo ya kanjedza.+ Oweruza Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:13 Nsanja ya Olonda,3/15/1997, tsa. 29
13 Kuwonjezera apo, anachititsa kuti Aamoni+ ndi Aamaleki+ alimbane ndi Aisiraeli. Iwo anamenyana ndi Aisiraeliwo nʼkulanda mzinda wa mitengo ya kanjedza.+