-
Oweruza 3:20Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
20 Ehudi anayandikira mfumuyo ili yokhayokha mʼchipinda chozizira bwino chapadenga. Ndiyeno ananena kuti: “Uthenga umene ndili nawo ndi wochokera kwa Mulungu.” Atatero, mfumuyo inanyamuka pampando wake wachifumu.
-