-
Oweruza 3:24Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
24 Iye atatuluka, atumiki a Egiloni anafika ndipo anapeza kuti zitseko za chipinda chapadenga ndi zokhoma. Ndiyeno anati: “Ayenera kuti akudzithandiza mʼchipinda chozizira bwino chamkati.”
-