Oweruza 3:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Atafika kumeneko analiza lipenga la nyanga ya nkhosa+ mʼdera lamapiri la Efuraimu.+ Ndiyeno Aisiraeli anatsika naye limodzi kuchoka mʼdera lamapirilo ndipo iye ankawatsogolera.
27 Atafika kumeneko analiza lipenga la nyanga ya nkhosa+ mʼdera lamapiri la Efuraimu.+ Ndiyeno Aisiraeli anatsika naye limodzi kuchoka mʼdera lamapirilo ndipo iye ankawatsogolera.