Oweruza 3:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Pambuyo pa Ehudi panabwera Samagara+ mwana wa Anati. Ameneyu anapha amuna 600 a Chifilisiti+ ndi ndodo yotosera ngʼombe pozitsogolera.+ Ameneyunso anapulumutsa Isiraeli.
31 Pambuyo pa Ehudi panabwera Samagara+ mwana wa Anati. Ameneyu anapha amuna 600 a Chifilisiti+ ndi ndodo yotosera ngʼombe pozitsogolera.+ Ameneyunso anapulumutsa Isiraeli.